Ezara 9:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nandisonkhanira ali yense wakunjenjemera pa mau a Mulungu wa Israyeli, cifukwa ca kulakwa kwa iwo a ndende; ndipo ndinakhala m'kudabwa mpaka nsembe yamadzulo.

Ezara 9

Ezara 9:1-7