Ezara 5:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anadza Sezibazara yemweyo namanga maziko a nyumba ya Mulungu iri m'Yerusalemu; ndipo kuyambira pomwepo kufikira tsopano irimkumangidwa, koma siinatsirizike.

Ezara 5

Ezara 5:14-17