Ezara 4:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo inalekeka nchito ya nyumba ya Mulungu yokhala ku Yerusalemu; nilekeka mpaka caka caciwiri ca ufumu wa Dariyo mfumu ya Perisiya.

Ezara 4

Ezara 4:16-24