Eksodo 9:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamenepo Yehova anati kwa Mose, Lowa kwa Farao, numuuze, Atero Yehova Mulungu wa Ahebri, Lola anthu anga amuke, kuti anditumikire.

2. Pakuti ukakana kuwalola amuke, ndi kuwagwira cigwiritsire,

Eksodo 9