Eksodo 8:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehovaanacita comweco; ndipo kunafika magulu a mizaza m'nyumba ya Farao, ndi m'nyumba za anyamata ace, ndi m'dziko lonse la Aigupto; dziko linaipatu cifukwa ca mizazayo.

Eksodo 8

Eksodo 8:15-32