Eksodo 7:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Muka kwa Farao m'mawa; taona, aturuka kumka kumadzi; nuime kumlinda m'mbali mwa nyanja; ndi ndodo idasanduka njokayo uigwire m'dzanja lako.

Eksodo 7

Eksodo 7:14-20