Eksodo 40:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ulongenso gomelo, nukonzerepo zokonzera zace; ulongenso coikapo nyalico, ndi kuyatsa nyali zace.

Eksodo 40

Eksodo 40:1-12