Eksodo 37:28-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

28. Ndipo anazipanga mphiko za mtengo wasitimu, nazikuta ndi golidi.

29. Anapanganso mafuta opatulika akudzoza nao, ndi cofukiza coona ca pfungo lokoma, mwa macitidwe a wosanganiza.

Eksodo 37