Eksodo 34:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anapita pamaso pace, napfuula, Yehova, Yehova, Mulungu wacifundo ndi wacisomo, wolekereza, ndi wa ukoma mtima wocuruka, ndi wacoonadi;

Eksodo 34

Eksodo 34:1-16