Eksodo 34:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anakhala pomwepo ndi Yehova masiku makumi anai, usana ndi usiku; sanadya mkate kapena kumwa madzi. Ndipo analembera pa magomewo mau a panganolo, mau khumiwo.

Eksodo 34

Eksodo 34:25-29