Eksodo 34:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Dzisungire cimene Ine ndikuuza lero lino: taona, ndiingitsa pamaso pako Aamori ndi Akanani, ndi Ahiti ndi Aperizi, ndi Ahivi, ndi Ayebusi.

Eksodo 34

Eksodo 34:8-16