Eksodo 34:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Mose, Dzisemere magome awiri amiyala onga oyamba aja; ndipo ndidzalembera pa magomewo mau omwewo anali pa magome oyambawo, amene unawaswa.

Eksodo 34

Eksodo 34:1-3