Eksodo 31:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Za amisiri opanga nchitoyi, Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti,

2. Taona ndaitana ndi kumchula dzina lace, Bezaleli, mwana wa Uri, mwana wa Huri, wa pfuke la Yuda;

Eksodo 31