Eksodo 30:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Asawatsanulire pa thupi la munthu; kapena musakonza ena onga awa, mwa makonzedwe ace; awa ndiwo opatulika, muwayese opatulika.

Eksodo 30

Eksodo 30:29-38