Eksodo 30:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo uzilandira ndarama za coteteza kwa ana a Israyeli, ndi kuzipereka pa nchito ya cihema cokomanako; kuti zikhale cikumbutso ca ana a Israyeli pamaso pa Yehova, kucita coteteza ca miyoyo yanu.

Eksodo 30

Eksodo 30:10-23