Eksodo 30:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ici acipereke, yense wakupita kwa owerengedwa; limodzi la magawo awiri a sekeli, monga sekeli la malo opatulika; (sekeli ndilo magera makumi awiri) limodzi la magawo awiri a sekeli, ndilo copereka ca Yehova.

Eksodo 30

Eksodo 30:7-16