Eksodo 3:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anati kwa Mulungu, Onani, pakufika ine kwa ana a Israyeli, ndi kunena nao, Mulungu wa makolo anu wandituma kwa inu; ndipo akakanena ndi ine, Dzina lace ndani? ndikanena nao ciani?

Eksodo 3

Eksodo 3:5-15