Eksodo 27:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo uzipanga nyanga zace pa ngondya zace zinai; nyanga zace zikhale zoturuka m'mwemo: nulikute ndi mkuwa:

Eksodo 27

Eksodo 27:1-9