Eksodo 21:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

akaukanso, nakayendayenda pabwalo ndi ndodo yace, womkanthayo azikhala womasuka; pakutsotsa pace pokha azimbwezera, namcizitse konse.

Eksodo 21

Eksodo 21:10-28