Eksodo 18:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anafotokozera mpongozi wace zonse Yehova adazicitira Farao ndi Aaigupto cifukwa ca Israyeli; ndi mabvuto onse anakomana nao panjira, ndi kuti Yehova adawalanditsa.

Eksodo 18

Eksodo 18:1-16