Eksodo 14:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzalimbitsa mtima wace wa Farao kuti awalondole; ndipo ndidzalemekezedwa pa Farao ndi pa nkhondo yace yonse; pamenepo Aaigupto adzadziwa kuti Ine ndine Yehova, Ndipo anacita comweco.

Eksodo 14

Eksodo 14:1-12