Eksodo 14:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza madziwo anabwerera, namiza magareta ndi apakavalo, ndiwo nkhondo yonse ya Farao imene idalowa pambuyo pao m'nyanja; sanatsala wa iwowa ndi mmodzi yense.

Eksodo 14

Eksodo 14:24-31