Eksodo 1:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. NDIPO maina a ana a Israyeli, amene analowa m'Aigupto ndi Yakobo ndi awa, analowa munthu ndi banja lace:

2. Rubeni, Simeoni, Levi ndi Yuda;

3. Isakara, Zebuloni, ndi Benjamini;

4. Dani ndi Nafitali, Gadi ndi Aseri.

Eksodo 1