Deuteronomo 5:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova ananena mau awa kwa msonkhano wanu wonse, m'phirimo ali pakati pa moto, pamtambo, pamdima bii, ndi mau akuru; osaonjezapo kanthu. Ndipo anawalembera pa magome awiri amiyala, nandipatsa awa.

Deuteronomo 5

Deuteronomo 5:18-30