Deuteronomo 5:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Mose anaitana Israyeli wonse, nanena nao, Tamverani, Israyeli, malemba ndi maweruzo ndinenawa m'makutu mwanu lero, kuti muwaphunzire, ndi kusamalira kuwacita.

2. Yehova Mulungu wathu anapangana nafe cipangano m'Horebe.

Deuteronomo 5