Deuteronomo 4:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, Israyeli, dioloketu tamverani malemba ndi maweruzo, amene ndikuphunzitsani muwacite; kuti mukhale ndi moyo, ndi kulowa, ndi kulandira dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu akupatsani.

Deuteronomo 4

Deuteronomo 4:1-11