Deuteronomo 32:49 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kwera m'phiri muno mwa Abarimu, phiri la Nebo, lokhala m'dziko la Moabu, popenyana ndi Yeriko; nupenye dziko la Kanani, limene ndipereka kwa ana a Israyeli likhale lao lao;

Deuteronomo 32

Deuteronomo 32:44-52