Deuteronomo 32:43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kondwerani, amitundu inu, ndi anthu ace;Adzalipsira mwazi wa atumiki ace,Adzabwezera cilango akumuukira,Nadzafafanizira zoipa dziko lace, ndi anthu ace.

Deuteronomo 32

Deuteronomo 32:37-47