Deuteronomo 31:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova adzawacitira monga anacitira Sihoni ndi Ogi, mafumu a Aamori, ndi dziko lao limene analiononga.

Deuteronomo 31

Deuteronomo 31:1-12