Deuteronomo 31:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano mudzilemberere nyimbo iyi, ndi kuphunzitsa ana a Israyeli iyi: mulike m'kamwa mwao, kuti nyimbo iyi indicitire mboni yotsutsa ana a Israyeli.

Deuteronomo 31

Deuteronomo 31:17-28