Deuteronomo 28:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova adzakulamulirani dalitso m'nkhokwe zanu, ndi m'zonse muturutsirako dzanja lanu; ndipo adzakudalitsani m'dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani,

Deuteronomo 28

Deuteronomo 28:2-12