Deuteronomo 28:66 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo moyo wanu udzakhala wanjiranjira pamaso panu, ndipo mudzacita mantha usiku ndi usana, osakhazika mtima za moyo wanu.

Deuteronomo 28

Deuteronomo 28:61-68