Deuteronomo 28:48 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa cace mudzatumikira adani anu amene Yehova adzakutumizirani, ndi njala, ndi ludzu, ndi usiwa, ndi kusowa zinthu zonse; ndipo adzaika goli lacitsulo pakhosi panu, kufikira atakuonongani.

Deuteronomo 28

Deuteronomo 28:38-56