Deuteronomo 28:40-42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

40. Mudzakhala nayo mitengo yaazitona m'malire anu onset osadzola mafuta; popeza zipatso za mitengo yaazitona zidzapululuka.

41. Mudzabala ana amuna ndi akazi, osakhala nao, popeza adzalowa ukapolo.

42. Mitengo yanu yonse ndi zipatso za nthaka yanu zidzakhala zao zao za dzombe.

Deuteronomo 28