Deuteronomo 26:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzali, utakalowa m'dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani likhale colowa canu, ndipo mwacilandira ndi kukhala m'mwemo;

Deuteronomo 26

Deuteronomo 26:1-4