Deuteronomo 24:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mutachera m'munda wanu wamphesa, musakunkha pambuyo panu; zikhale za mlendo, za mwana wamasiye, ndi za mkazi wamasiye.

Deuteronomo 24

Deuteronomo 24:15-22