Deuteronomo 2:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo muja tinalanda midzi yace yonse; ndipo tinaononga konse midzi yonse, amuna ndi akazi ndi ana; sitinasiyapo ndi mmodzi yense.

Deuteronomo 2

Deuteronomo 2:31-37