Deuteronomo 18:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Asapezeke mwa inu munthu wakupitiriza mwana wace wamwamuna kapena mwana wace wamkazi ku mota wa ula, wosamalira mitambo, kapena wosamalira kulira kwa mbalame, kapena wanyanga.

Deuteronomo 18

Deuteronomo 18:6-12