Danieli 9:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuyamba iwe mapembedzero ako, linaturuka lamulo; ndipo ndadza ine kukufotokozera; pakuti ukondedwa kwambiri; zindikira tsono mau awa, nulingirire masomphenyawo.

Danieli 9

Danieli 9:21-27