Danieli 4:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mfumu Nebukadinezara, kwa anthu, mitundu ya anthu, ndi a manenedwe okhala pa dziko lonse lapansi: Mtendere ucurukire inu.

2. Candikomera kuonetsa zizindikilo ndi zozizwa, zimene anandicitira Mulungu Wam'mwambamwamba.

Danieli 4