Danieli 2:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Akasidi anati kwa mfumu m'Ciaramu, Mfumu, mukhale ndi moyo cikhalire: mufotokozere anyamata anu lotoli, ndipo tidzakuuzani kumasulira kwace.

Danieli 2

Danieli 2:1-14