Danieli 12:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ine Danieli ndinapenya, ndipo taonani, anaimapo awiri ena, wina m'mphepete mwa mtsinje tsidya lino, ndi mnzace m'mphepete mwa mtsinje tsidya lija.

Danieli 12

Danieli 12:1-9