Cibvumbulutso 6:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene adamasula cizindikilo cacisanu, ndinaona pansi pa guwa la nsembe mizimu ya iwo adaphedwa cifukwa ca mau a Mulungu, ndi cifukwa ca umboni umene anali nao:

Cibvumbulutso 6

Cibvumbulutso 6:5-16