Cibvumbulutso 3:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kwa mngelo wa Mpingo wa ku Filadelfeya lemba;Izi anena iye amene ali Woyera, iye amene ali Woona, iye wakukhala naco cifungulo ca Davide, iye wotsegula, ndipo palibe wina atseka; iye wotseka, ndipo palibe wina atsegula:

Cibvumbulutso 3

Cibvumbulutso 3:1-14