Cibvumbulutso 22:20-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. Iye wakucitira umboni izi, anena, 4 Indetu; ndidza msanga. Amen; idzani, Ambuye Yesu.

21. 5 Cisomo ca Ambuye Yesu cikhale ndi oyera mtima onse, Amen.

Cibvumbulutso 22