Cibvumbulutso 22:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ine Yesu ndatuma mngelo wanga kukucitirani umboni za izi m'Mipingo. Ine ndine muzo ndi mbadwa ya Davide, nyenyezi yonyezimira ya nthanda.

Cibvumbulutso 22

Cibvumbulutso 22:8-20