Aroma 4:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo tsono tidzanena kuti Abrahamu, kholo lathu monga mwa thupi, analandira ciani?

2. Pakuti ngati Abrahamu anayesedwa wolungama cifukwa ca nchito, iye akhala naco codzitamandira; koma kulinga kwa Mulungu ai.

Aroma 4