Aroma 3:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo potero Myuda aposa Dinji? Kapena mdulidwe upindulanji?

2. Zambiri monse monse: coyamba, kuti mau a Mulungu anaperekedwa kwa iwo.

Aroma 3