Aroma 15:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndikudandaulirani, abale, ndi Ambuye wathu Yesu Kristu, ndi cikondi ca Mzimu, kuti 5 mudzalimbike pamodzi ndi ine m'mapemphero anu kwa Mulungu cifukwa ca ine;

Aroma 15

Aroma 15:28-33