Aroma 14:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti tingakhale tiri ndi moyo, tikhalira Ambuye moyo; kapena tikafa, tifera Ambuye; cifukwa cace tingakhale tiri ndi moyo, kapena tikafa, tikhala ace a Ambuye.

Aroma 14

Aroma 14:1-15